Nehemiya 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kuti akhala kumbali yake chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wa Tobia anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wa Berekiya.
18 Anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kuti akhala kumbali yake chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wa Tobia anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wa Berekiya.