Nehemiya 7:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri koma sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, komanso kuti anali Aisiraeli kapena ayi,+ ndi awa:
61 Amene anachokera ku Tele-mela, Tele-harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri koma sanathe kufotokoza mzere wa makolo awo ndi kumene anachokera, komanso kuti anali Aisiraeli kapena ayi,+ ndi awa: