Nehemiya 7:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Panalinso atsogoleri ena a nyumba za makolo amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchitoyo kumalo osungira chuma. Iwo anapereka ndalama za dalakima zagolide 20,000 ndi ndalama za mina* zasiliva 2,200.
71 Panalinso atsogoleri ena a nyumba za makolo amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchitoyo kumalo osungira chuma. Iwo anapereka ndalama za dalakima zagolide 20,000 ndi ndalama za mina* zasiliva 2,200.