Nehemiya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu onse anasonkhana mogwirizana mʼbwalo lalikulu kutsogolo kwa Geti la Kumadzi.+ Anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba* kuti abweretse buku la Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova analamula Aisiraeli kuti azitsatira.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,2/2016, tsa. 3
8 Anthu onse anasonkhana mogwirizana mʼbwalo lalikulu kutsogolo kwa Geti la Kumadzi.+ Anthuwo anauza Ezara+ wokopera Malemba* kuti abweretse buku la Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova analamula Aisiraeli kuti azitsatira.+