Nehemiya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Ezara wansembe anapititsa buku la Chilamulo kugulu la anthuwo.+ Panali amuna, akazi komanso aliyense amene akanatha kumvetsa zimene zikunenedwa. Limeneli linali tsiku loyamba la mwezi wa 7.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, tsa. 20
2 Choncho Ezara wansembe anapititsa buku la Chilamulo kugulu la anthuwo.+ Panali amuna, akazi komanso aliyense amene akanatha kumvetsa zimene zikunenedwa. Limeneli linali tsiku loyamba la mwezi wa 7.+