Nehemiya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Ezara anatamanda Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse ananena kuti, “Ame! Ame!”*+ ndipo anakweza manja awo mʼmwamba. Ndiyeno anthuwo anagwada nʼkuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo kufika pansi.
6 Kenako Ezara anatamanda Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse ananena kuti, “Ame! Ame!”*+ ndipo anakweza manja awo mʼmwamba. Ndiyeno anthuwo anagwada nʼkuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo kufika pansi.