Nehemiya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno anapeza kuti mʼChilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose analembamo kuti Aisiraeli azikhala mʼmisasa pa nthawi yachikondwerero mʼmwezi wa 7.+
14 Ndiyeno anapeza kuti mʼChilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose analembamo kuti Aisiraeli azikhala mʼmisasa pa nthawi yachikondwerero mʼmwezi wa 7.+