Nehemiya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho gulu lonse la anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo anamanga misasa nʼkukhala mʼmisasayo. Anthu anasangalala kwambiri+ chifukwa Aisiraeli anali asanachitepo zimenezi kuchokera mu nthawi ya Yoswa+ mwana wa Nuni, mpaka nthawi imeneyi.
17 Choncho gulu lonse la anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo anamanga misasa nʼkukhala mʼmisasayo. Anthu anasangalala kwambiri+ chifukwa Aisiraeli anali asanachitepo zimenezi kuchokera mu nthawi ya Yoswa+ mwana wa Nuni, mpaka nthawi imeneyi.