Nehemiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu Aisiraeli anasonkhana pamodzi ndipo anasala kudya atavala ziguduli komanso atadzithira dothi kumutu.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, tsa. 31
9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu Aisiraeli anasonkhana pamodzi ndipo anasala kudya atavala ziguduli komanso atadzithira dothi kumutu.+