Nehemiya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anaimirirabe ndipo anawerenga mokweza buku la Chilamulo+ cha Yehova Mulungu wawo kwa maola atatu. Kwa maola enanso atatu anaulula machimo awo ndiponso kugwadira Yehova Mulungu wawo. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Nsanja ya Olonda,10/15/2013, tsa. 22
3 Iwo anaimirirabe ndipo anawerenga mokweza buku la Chilamulo+ cha Yehova Mulungu wawo kwa maola atatu. Kwa maola enanso atatu anaulula machimo awo ndiponso kugwadira Yehova Mulungu wawo.