-
Nehemiya 9:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo Yesuwa, Kadimiyeli, Bani, Hasabineya, Serebiya, Hodiya, Sebaniya ndi Petahiya, omwe anali Alevi, anati: “Imirirani ndipo mutamande Yehova Mulungu wanu mpaka kalekale.*+ Inu Mulungu wathu, anthuwa atamande dzina lanu laulemerero, lomwe ndi lalikulu kuposa dalitso ndiponso chitamando chilichonse.
-