Nehemiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munagawa nyanja pamaso pawo ndipo anadutsa panthaka youma.+ Anthu amene ankawathamangitsa munawaponya pansi pa nyanja ngati mwala woponyedwa mʼmafunde amphamvu.+
11 Munagawa nyanja pamaso pawo ndipo anadutsa panthaka youma.+ Anthu amene ankawathamangitsa munawaponya pansi pa nyanja ngati mwala woponyedwa mʼmafunde amphamvu.+