Nehemiya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masana munkawatsogolera ndi chipilala cha mtambo ndipo usiku munkawatsogolera ndi chipilala cha moto kuti uziwaunikira njira imene ankayenera kudutsa.+
12 Masana munkawatsogolera ndi chipilala cha mtambo ndipo usiku munkawatsogolera ndi chipilala cha moto kuti uziwaunikira njira imene ankayenera kudutsa.+