Nehemiya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale pamene anapanga chifaniziro chachitsulo cha mwana wa ngʼombe nʼkuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu amene anakutulutsani ku Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,
18 Ngakhale pamene anapanga chifaniziro chachitsulo cha mwana wa ngʼombe nʼkuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu amene anakutulutsani ku Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,