Nehemiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino kuti akhale anzeru.+ Simunawamane mana+ ndipo pamene anali ndi ludzu munawapatsa madzi.+
20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino kuti akhale anzeru.+ Simunawamane mana+ ndipo pamene anali ndi ludzu munawapatsa madzi.+