Nehemiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo munachulukitsa ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Kenako munawalowetsa mʼdziko limene munalonjeza makolo awo kuti adzalowamo nʼkulitenga kukhala lawo.+
23 Ndipo munachulukitsa ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Kenako munawalowetsa mʼdziko limene munalonjeza makolo awo kuti adzalowamo nʼkulitenga kukhala lawo.+