Nehemiya 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho ana awo analowa nʼkutenga dzikolo.+ Munagonjetsa Akanani,+ anthu amʼdzikolo ndipo munawapereka mʼmanja mwawo. Munaperekanso mafumu a Akananiwo ndi anthu amʼdzikolo kwa Aisiraeli kuti awachitire zimene akufuna.
24 Choncho ana awo analowa nʼkutenga dzikolo.+ Munagonjetsa Akanani,+ anthu amʼdzikolo ndipo munawapereka mʼmanja mwawo. Munaperekanso mafumu a Akananiwo ndi anthu amʼdzikolo kwa Aisiraeli kuti awachitire zimene akufuna.