Nehemiya 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Munawalezera mtima+ kwa zaka zambiri ndipo munapitiriza kuwachenjeza pogwiritsa ntchito mzimu wanu kudzera mwa aneneri anu, koma anakana kumvera. Kenako munawapereka mʼmanja mwa anthu amʼdzikolo.+
30 Munawalezera mtima+ kwa zaka zambiri ndipo munapitiriza kuwachenjeza pogwiritsa ntchito mzimu wanu kudzera mwa aneneri anu, koma anakana kumvera. Kenako munawapereka mʼmanja mwa anthu amʼdzikolo.+