Nehemiya 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ngakhale pamene ankalamuliridwa ndi mafumu awo ndipo ankadalitsidwa kwambiri komanso ankakhala mʼdziko lalikulu ndi lachonde limene munawapatsa, iwo sankakutumikirani+ ndipo sanasiye kuchita zoipa.
35 Ngakhale pamene ankalamuliridwa ndi mafumu awo ndipo ankadalitsidwa kwambiri komanso ankakhala mʼdziko lalikulu ndi lachonde limene munawapatsa, iwo sankakutumikirani+ ndipo sanasiye kuchita zoipa.