Nehemiya 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pano ndife akapolo.+ Ndife akapolo mʼdziko limene munapatsa makolo athu kuti adye zipatso zake ndi zinthu zake zabwino.
36 Pano ndife akapolo.+ Ndife akapolo mʼdziko limene munapatsa makolo athu kuti adye zipatso zake ndi zinthu zake zabwino.