Nehemiya 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho chifukwa cha zimenezi, tikuchita pangano lodalirika+ lochita kulemba ndipo akalonga athu, Alevi athu ndi ansembe athu atsimikizira panganoli ndi chidindo chawo.”+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:38 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, tsa. 21
38 Choncho chifukwa cha zimenezi, tikuchita pangano lodalirika+ lochita kulemba ndipo akalonga athu, Alevi athu ndi ansembe athu atsimikizira panganoli ndi chidindo chawo.”+