29 anagwirizana ndi abale awo, anthu otchuka. Iwo analumbira kuti azitsatira Chilamulo cha Mulungu woona chimene chinaperekedwa kudzera mwa Mose mtumiki wa Mulungu woona komanso kuti azitsatira mosamala malamulo onse, ziweruzo ndi mfundo za Yehova Ambuye wathu.