Nehemiya 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Otsatirawa ndi atsogoleri a chigawo cha Yuda amene ankakhala ku Yerusalemu, (Aisiraeli ena onse, ansembe, Alevi, atumiki apakachisi*+ ndiponso ana a atumiki a Solomo+ ankakhala mʼmizinda ina ya Yuda. Aliyense ankakhala pamalo ake mumzinda wake.+
3 Otsatirawa ndi atsogoleri a chigawo cha Yuda amene ankakhala ku Yerusalemu, (Aisiraeli ena onse, ansembe, Alevi, atumiki apakachisi*+ ndiponso ana a atumiki a Solomo+ ankakhala mʼmizinda ina ya Yuda. Aliyense ankakhala pamalo ake mumzinda wake.+