Nehemiya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ omwe anali mʼgulu la atsogoleri a Alevi. Amenewa ankayangʼanira ntchito yapanja pa nyumba ya Mulungu woona.
16 Panalinso Sabetai+ ndi Yozabadi,+ omwe anali mʼgulu la atsogoleri a Alevi. Amenewa ankayangʼanira ntchito yapanja pa nyumba ya Mulungu woona.