Nehemiya 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alonda apageti anali Akubu, Talimoni+ ndi abale awo amene ankalondera mʼmageti. Onse pamodzi analipo 172.
19 Alonda apageti anali Akubu, Talimoni+ ndi abale awo amene ankalondera mʼmageti. Onse pamodzi analipo 172.