Nehemiya 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atumiki apakachisi*+ ankakhala ku Ofeli+ ndipo Ziha ndi Gisipa ankayangʼanira atumiki apakachisiwo.
21 Atumiki apakachisi*+ ankakhala ku Ofeli+ ndipo Ziha ndi Gisipa ankayangʼanira atumiki apakachisiwo.