Nehemiya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mʼmasiku a Yoyakimu anthu awa ndi amene anali ansembe, atsogoleri a nyumba za makolo: Woimira nyumba ya Seraya+ anali Meraya, woimira nyumba ya Yeremiya anali Hananiya.
12 Mʼmasiku a Yoyakimu anthu awa ndi amene anali ansembe, atsogoleri a nyumba za makolo: Woimira nyumba ya Seraya+ anali Meraya, woimira nyumba ya Yeremiya anali Hananiya.