Nehemiya 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso mʼmadera a ku Geba+ ndi ku Azimaveti,+ chifukwa oimbawo anamanga midzi yawo kuzungulira Yerusalemu yense.
29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso mʼmadera a ku Geba+ ndi ku Azimaveti,+ chifukwa oimbawo anamanga midzi yawo kuzungulira Yerusalemu yense.