Nehemiya 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Panalinso Semaya, Azareli, Milalai, Gilelai, Maai, Netaneli, Yuda ndi Haneni, abale ake a Zekariya. Anali ndi zipangizo zoimbira za Davide,+ munthu wa Mulungu woona, ndipo amene ankawatsogolera anali Ezara+ wokopera Malemba.*
36 Panalinso Semaya, Azareli, Milalai, Gilelai, Maai, Netaneli, Yuda ndi Haneni, abale ake a Zekariya. Anali ndi zipangizo zoimbira za Davide,+ munthu wa Mulungu woona, ndipo amene ankawatsogolera anali Ezara+ wokopera Malemba.*