Nehemiya 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anadutsanso pamwamba pa Geti la Efuraimu,+ Geti la Mzinda Wakale,+ Geti la Nsomba+ mpaka kukafika pa Nsanja ya Hananeli,+ Nsanja ya Meya ndi ku Geti la Nkhosa,+ ndipo anaima pa Geti la Alonda.
39 Anadutsanso pamwamba pa Geti la Efuraimu,+ Geti la Mzinda Wakale,+ Geti la Nsomba+ mpaka kukafika pa Nsanja ya Hananeli,+ Nsanja ya Meya ndi ku Geti la Nkhosa,+ ndipo anaima pa Geti la Alonda.