-
Nehemiya 12:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Ansembe ndi Alevi anayamba kugwira ntchito ya Mulungu wawo ndiponso kusunga lamulo lakuti azikhala oyera, ngati mmene ankachitira oimba ndi alonda apageti, mogwirizana ndi malangizo a Davide ndi mwana wake Solomo.
-