Nehemiya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinazindikiranso kuti Alevi sankapatsidwa magawo awo, moti Alevi+ ndiponso oimba amene ankatumikira anachoka,+ ndipo aliyense anapita kumunda wake.+
10 Ndinazindikiranso kuti Alevi sankapatsidwa magawo awo, moti Alevi+ ndiponso oimba amene ankatumikira anachoka,+ ndipo aliyense anapita kumunda wake.+