Nehemiya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinadzudzula atsogoleriwo+ ndipo ndinawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani nyumba ya Mulungu woona yasiyidwa chonchi?”+ Kenako ndinawasonkhanitsa nʼkuwabwezera pa ntchito zawo. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,8/15/2013, ptsa. 4-5
11 Choncho ndinadzudzula atsogoleriwo+ ndipo ndinawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani nyumba ya Mulungu woona yasiyidwa chonchi?”+ Kenako ndinawasonkhanitsa nʼkuwabwezera pa ntchito zawo.