-
Nehemiya 13:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno ndinaika Selemiya wansembe, Zadoki wokopera Malemba* ndi Pedaya Mlevi, kuti aziyangʼanira zipinda zosungira katundu. Ndipo Hanani mwana wa Zakuri amene anali mwana wa Mataniya, anali wachiwiri wawo chifukwa anthuwa ankaonedwa kuti ndi okhulupirika. Iwowa anapatsidwa udindo wogawa zinthu kwa abale awo.
-