-
Nehemiya 13:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Masiku amenewo ndinaona anthu ku Yuda akuponda moponderamo mphesa pa tsiku la Sabata.+ Ankabweretsa mbewu ndipo ankazikweza pa abulu. Ankabweretsanso vinyo, mphesa, nkhuyu ndi katundu wosiyanasiyana ku Yerusalemu pa tsiku la Sabata.+ Choncho ndinawadzudzula pa nkhani yogulitsa zinthu pa tsiku limenelo.*
-