Nehemiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu a ku Turo amene ankakhala mumzindawu ankabweretsa nsomba ndi zinthu zosiyanasiyana nʼkumagulitsa kwa anthu a ku Yuda ndiponso mu Yerusalemu pa tsiku la Sabata.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 1 2020 tsa. 7
16 Anthu a ku Turo amene ankakhala mumzindawu ankabweretsa nsomba ndi zinthu zosiyanasiyana nʼkumagulitsa kwa anthu a ku Yuda ndiponso mu Yerusalemu pa tsiku la Sabata.+