-
Nehemiya 13:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Hafu ya ana awo aamuna ankalankhula Chiasidodi ndipo hafu ina inkalankhula zilankhulo za anthu a mitundu ina koma panalibe amene ankatha kulankhula chilankhulo cha Ayuda.
-