5 Zimenezi zitatha, mfumu inakonza phwando la masiku 7 pabwalo la nyumba yake pomwe anadzalapo maluwa. Phwandoli inakonzera anthu onse, kaya olemekezeka kapena anthu wamba, amene ankakhala kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.