-
Esitere 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Panali makatani a nsalu zoyera, makatani opangidwa ndi thonje labwino kwambiri ndi makatani abuluu. Makataniwo anawamanga ndi zingwe zopangidwa ndi nsalu zabwino kwambiri ndipo anawapachika mʼmikombero yasiliva yokulungidwa ndi ulusi wapepo. Mikomberoyo anaikoleka pa zipilala za miyala ya mabo. Panalinso mipando yagolide ndi siliva yokhala ngati mabedi imene inali pakhonde la miyala ya pofeli,* miyala yoyera ya mabo, ngale ndi miyala yakuda ya mabo.
-