-
Esitere 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Panali vinyo yemwe anthu ankamwera mʼmakapu agolide. Kapu iliyonse inali yosiyana ndi inzake, ndipo vinyo amene mfumu inapereka anali wambiri, mogwirizana ndi chuma cha mfumuyo.
-