-
Esitere 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 kuti akatenge Mfumukazi Vasiti nʼkubwera naye kwa mfumu atavala duku lachifumu, kuti anthu onse ndi akalonga aone kukongola kwake, chifukwa analidi wokongola kwambiri.
-