-
Esitere 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno mfumu inalankhula ndi amuna anzeru, odziwa miyambo ya masiku amenewo. (Zimenezi zinkathandiza kuti nkhani zokhudza mfumu zifike kwa anthu onse odziwa malamulo komanso milandu.
-