Esitere 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alangizi amene ankakhala pafupi ndi mfumu anali Karisena, Setara, Adimata, Tarisi, Meresi, Marisena ndi Memukani, akalonga 7+ a Perisiya ndi Mediya, amene ankafika kwa mfumu komanso anali ndi maudindo akuluakulu mu ufumuwo.)
14 Alangizi amene ankakhala pafupi ndi mfumu anali Karisena, Setara, Adimata, Tarisi, Meresi, Marisena ndi Memukani, akalonga 7+ a Perisiya ndi Mediya, amene ankafika kwa mfumu komanso anali ndi maudindo akuluakulu mu ufumuwo.)