Esitere 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moredikayi ndi anthu ena anatengedwa ku Yerusalemu kupita ku ukapolo pamodzi ndi Yekoniya*+ mfumu ya Yuda, amene Nebukadinezara mfumu ya Babulo anamutenga kupita naye ku ukapolo.
6 Moredikayi ndi anthu ena anatengedwa ku Yerusalemu kupita ku ukapolo pamodzi ndi Yekoniya*+ mfumu ya Yuda, amene Nebukadinezara mfumu ya Babulo anamutenga kupita naye ku ukapolo.