-
Esitere 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Hegai anasangalala naye mtsikanayu moti ankamukomera mtima.* Choncho nthawi yomweyo anakonza za mafuta okongoletsa oti azipakidwa+ komanso chakudya choti azipatsidwa. Anamupatsanso atsikana 7 amene anachita kuwasankha kuchokera kunyumba ya mfumu. Kenako anamusamutsa pamodzi ndi atsikanawo nʼkuwapatsa malo abwino kwambiri mʼnyumba ya akaziyo.
-