Esitere 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Esitere sananene za mtundu wa anthu ake+ kapena za abale ake, chifukwa Moredikayi+ anali atamulangiza kuti asauze aliyense.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Tsanzirani, tsa. 130 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 20
10 Esitere sananene za mtundu wa anthu ake+ kapena za abale ake, chifukwa Moredikayi+ anali atamulangiza kuti asauze aliyense.+