Esitere 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumu inakonda kwambiri Esitere kuposa akazi ena onse, moti inasangalala naye ndipo inaona kuti ndi wabwino* kuposa anamwali ena onse. Choncho mfumu inamuveka duku lachifumu kumutu kwake nʼkumuika kukhala mfumukazi+ mʼmalo mwa Vasiti.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 31
17 Ndiyeno mfumu inakonda kwambiri Esitere kuposa akazi ena onse, moti inasangalala naye ndipo inaona kuti ndi wabwino* kuposa anamwali ena onse. Choncho mfumu inamuveka duku lachifumu kumutu kwake nʼkumuika kukhala mfumukazi+ mʼmalo mwa Vasiti.+