-
Esitere 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mʼmasiku amenewo, pamene Moredikayi ankakhala pageti la mfumu, Bigitana ndi Teresi, omwe anali nduna ziwiri zapanyumba ya mfumu, omwenso anali alonda apakhomo, anakwiya ndipo anakonza zoti aphe Mfumu Ahasiwero.
-