Esitere 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho nkhaniyi inafufuzidwa ndipo zinadziwika kuti inali yoona, moti Bigitana ndi Teresi anapachikidwa pamtengo. Zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu mʼbuku la mbiri ya masiku amenewo.+
23 Choncho nkhaniyi inafufuzidwa ndipo zinadziwika kuti inali yoona, moti Bigitana ndi Teresi anapachikidwa pamtengo. Zimenezi zinalembedwa pamaso pa mfumu mʼbuku la mbiri ya masiku amenewo.+