Esitere 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mfumu Ahasiwero anakweza pa udindo Hamani+ mwana wa Hamedata mbadwa ya Agagi,+ ndipo anamupatsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse a mfumuyo.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Tsanzirani, tsa. 131 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 21
3 Kenako Mfumu Ahasiwero anakweza pa udindo Hamani+ mwana wa Hamedata mbadwa ya Agagi,+ ndipo anamupatsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse a mfumuyo.+